Changamire M’zizi (Kantini Samson) is a Zambian poet, a development educationalist, and a cultural historian. He is interested in the aims, the strategies, and the content of the socialization and transformative processes that they ought to have in place to create, promote and raise the critical consciousness of wholeness in low-resourced environments in order to bridge the divide between the worlds of rich and poor, and the theory and practice for sustainable societies. He holds a Ph.D. in Education from Seoul National University, an MEd in Education and Development from The University of Zambia (UNZA), an MA in Literature, and a BA in Education (BAEd) also from UNZA. He has received a Certificate in Diplomatic Practice, Protocol, and Public Relations from the Zambia Institute of Diplomacy and International Studies (ZIDIS). Currently, He is Senior Programme Officer for Culture, Communication and Information at the Zambia National Commission for the United Nations Educational, Scientific and Cultural Organisation (UNESCO)

냔자어/체와어(Nyanja/Chewa) : 체와어(Chewa)는 말라위의 공용어이다. 니제르콩고어족에 속하며 냔자어(Nanja)로도 알려져 있다. 시인은 모어(母語)인 냔자어(Nyanja)/체와어(Chewa)로 이야기의 내용, 그 속의 인물들, 그것이 지니는 문화적 가치 등의 이미지와 격언과 비유를 표현한

.

 

Kambewa iyaye
Kambewa iyaye
Sikanganilume iyaye
Sikanganilume ine kambewa

Akulira Adada
Amama atengedwa ndi nkhani yamalaiti
Sadziwanso cikondi
Akuti malaiti
Afuna malaiti, safuna cikondi
Safuna cikondi, afuna malaiti

Adada akulira
Iwo sizesiko yopatsa malaiti
Koma amama, afuna malaiti
Ndi mlongo wanga, akuti malaiti
Koma nsima, kamtaka, saapika
Kapena Mpiru, uyu ndi usiru
Ndi malaiti otani akuletsa kupika
Khoswe akakhala pa mkate sapeka
Adada akwiya
Cikakhala coteka uyu koswe adzapeka
Nadyedwa monga mbewa yochedwa ntika

Adada akulira
Cikondi akwanisa osati malaiti
Zesiko malaiti iwo amasira
Popeza ndi tupamela
Dzina la Amama tsono ndi Pamela
Pamene pamala pomwe sipamera
Kuti abale afuna bebi-sita
Zaka zingopita iwo samita
Safuna cikondi akuti sicipimika
Afuna malaiti cifukwa ali ndi mita

Adada akulira…
Amama asowa ndi nkhani ya malaiti
Ife ndife anthu tisanakale amuna kapena akazi
Koma nkhani malaiti ilankhula zina
Akuti ndi akazi cifukwa ena ndi amuna
Umoyo si umuna kapena ukazi
Umoyo ndi unthu, unthu wa umunthu
Nzika zimodzi, dziko limodzi, cikondi cimodzi.

저작권자 © 더스쿠프 무단전재 및 재배포 금지

개의 댓글

0 / 400
댓글 정렬
BEST댓글
BEST 댓글 답글과 추천수를 합산하여 자동으로 노출됩니다.
댓글삭제
삭제한 댓글은 다시 복구할 수 없습니다.
그래도 삭제하시겠습니까?
댓글수정
댓글 수정은 작성 후 1분내에만 가능합니다.
/ 400

내 댓글 모음